0% found this document useful (0 votes)
10 views4 pages

Chichewa P II Marking Key

The document is a mock examination for the 2025 Malawi School Certificate of Education in Chichewa, covering various topics such as language functions, grammatical structures, and comprehension questions. It includes sections on conjunctions, prepositions, and verb tenses, as well as discussions on cultural and social issues. Additionally, it addresses reproductive health methods and the importance of individual rights and protections under the law.

Uploaded by

bah-72-20
Copyright
© © All Rights Reserved
We take content rights seriously. If you suspect this is your content, claim it here.
Available Formats
Download as PDF, TXT or read online on Scribd
0% found this document useful (0 votes)
10 views4 pages

Chichewa P II Marking Key

The document is a mock examination for the 2025 Malawi School Certificate of Education in Chichewa, covering various topics such as language functions, grammatical structures, and comprehension questions. It includes sections on conjunctions, prepositions, and verb tenses, as well as discussions on cultural and social issues. Additionally, it addresses reproductive health methods and the importance of individual rights and protections under the law.

Uploaded by

bah-72-20
Copyright
© © All Rights Reserved
We take content rights seriously. If you suspect this is your content, claim it here.
Available Formats
Download as PDF, TXT or read online on Scribd
You are on page 1/ 4

BWAILA CLUSTER MOCK EXAMINATIONS

2025 MALAWI SCHOOL CERTIFICATE OF EDUCATION EXAMINATION

CHICHEWA
PEPALA LACHIWIRI
CHIYEMBEKEZO CHA MAYANKHO

GAWO A
1. a. Ntchito za alumikizi.
i. Ndipo - Kulunzanitsa/ Kuphatikiza
ii. Osati - Kutayanitsa/ Kulekanitsa
iii. Chifukwa - Kusonyeza m’gwirizano
iv. Koma - Kupatula
v. Kuti - Kusonyeza m’gwirizano
b. Mitundu ya mimvekero
i. Psu - Mvekero wamaonekedwe
ii. nji - mvekero wamkhalidwe
iii. gubidi - mvekero wamchitidwe
iv. phofo - mvekero wamamvekedwe
v. chete - mvekero wamkhalidwe
2. a. Mitundu ya Aperekezi
i. Wosonyeza malo/mbali (mu, pa, kwa) - Ayika mu mbale
- Chili pa thandala
- Ndapititsa kwa eni ake
ii. wosonyeza umwini ( la, ya, wa) - Kope langa, Nkhokwe yawo, Mwana
wanga
iii. wosonyeza mgwirizano (Ali kuseri kwa mwala).
Ali ndi nzeru
iv. wosonyeza nthawi ( pa 19, kwa zaka zitatu mu December)
v. wosonyeza chipangizo (Abwera pa njinga.)

pg. 1
Amutuma ndi chikwanje.
b. Ntchito za “ndi”
i. Kukhala mvekero
Anamanga mtolo kuti ndi.
ii. Kukhala mneni
Malawi ndi dziko lokongola.
iii. Kukhala mperekezi
Jeputala wandimenya ndi ndodo.
3. a. Misintho ya aneni
i. limira
ii. limitsitsa
iii. limirana
iv. limitsa
v. limidwa
b. Ntchito za “ti”
i. Kukhala mgwirizanitsi wamchitidwantchito
ii. Kukhala tsinde lamneni
c. Nthawi za aneni
i. yatsopano yopitirira
Akudya nsima yosapsa
ii. yam’tsogolo yathayi yopitirira
Adzakhala akudya nsima yosapsa.
iii. Yakale
Adadya nsima yosapsa.
4. Akapandamneni ndi ntchito zawo
i Kubera anthu osauka
kukhala mchitantchito wamneni ‘ndi’

ii. Motomoto lero!


kusonyeza kukondwa

iii. Mwana waulemu

pg. 2
mchitidwantchito wadzindunji wamneni ‘amakonda’

iv. Aphunzitsi athu a Chichewa


mtsiriza tanthauzo lamneni ‘ndi’

v. Pa 2 August 2025
kusonyeza nthawi/kukamba zambiri za mneni ‘adabadwa’
GAWO B
Kuyankha mafunso a kumvetsa nkhani
5. a. i. kudali ku Dowa
ii. Amalume ake ndi omwe adamutenga kubwera ku Lilongwe.
iii. Azakhali ake amafuna agwire ntchito zolemetsa asadapite kusukulu, akalephera
amamulalatira kwambiri.
iv. Amalolera kulawira kwambiri kukalima ndi kusamba ku mtsinje asadapite kusukulu.
v. Anthu adawofotokozera mmene Pirirani amazunzikira.
vi. Kupilira
vii. Anyamata adali osuta chamba, atsikana adali achimasomaso.
viii. Adayamba kumunyoza ndi kumunenera zoipa.
ix. Adali chitsanzo cha makhalidwe abwino.
b. Kusanthula Chiyakhulo
i. Nkhwangwa - atsikana osakongola
Mbanje - chamba
Atsizinan’tole - akuba

ii. Adawauza - adawatsina khutu


Mtsikana wokongola - njole
GAWO C
Chifupikitso
6. UFULU WA CHIBADWIDWE PA CHITETEZO
Munthu ndi wotetezedwa ndi lamulo posaganizira kusiyana kulikonse./

Boma limateteza nzika zake/ komanso nzika za maiko ena./

pg. 3
Moyo umayamba usanabadwe./ Ngakhale mwana wosabadwa ndi wotetezedwa ndi
lamulo./ Munthu alibenso ufulu wodzipha/ ndipo akapulumutsidwa amazengedwa mlandu
wofuna kuchotsa moyo./
GAWO D
Chimasuliro
7. MITUNDU YA NJIRA ZAKULERA
Pali njira zopitirira zisanu ndi imodzi zomwe anthu amasankha polera masiku ano ndipo
zina mwa izo ndi jakisoni, makondomu (mpira wa amayi kapena abambo), mankhwala
akumwa, noropulanti, kutseka kwa abambo komanso kutseka kwa amayi.

Njira yomwe anthu amayigwiliritsa ntchito kwambiri ndi kondomu. Njirayi imateteza ku
matenda opatsirana pogonana, kuonjezerapo matenda a Edzi. Pamene makodomu akuteteza
ku matenda opatsirana pogonana, mabanja ambiri amawagwiritsa ntchito limodzi ndi njira
zina zakulera. Koma makondomu ndi ophweka kugwiritsa ntchito.

Kutseka kwa abambo ndi njira yokhalitsa (yamuyaya) ya abambo omwe atsimikiza kuti
sadzafunanso ana ena. Njirayi ndi yodalirika komanso siikhudza chilakolako chogonana
cha abambo.

Kutseka kwa abambo ndi njira yolera yokhalitsa ya abambo yomwe abambo omwe
atsimikiza kuti sakufunaso ana ena akhoza kugwiritsa ntchito. Njirayi ndi yodalilika
komanso siikhudza chilakolako chogonana cha abamvo.

CHIYEREKEZO CHA MAYANKHO PAPER 2 CHATHERA PANO

pg. 4

You might also like